Top·
Tidakumana Bwanji

Source:mwnation ↗
MMulungu amadalitsa anthu ake m’njira zodwabwitsa. Samuel Yohane, Mulungu adamuyendera mu njira yapadera. Mnyamatayu amaimba kwayala pa mpingo wa Nchalo Seventh-Day Adventist (SDA) m’boma la Chikwawa. M’chaka cha 2023, mnzake woimba naye kwayala adafika ku mpingoko ndi m’bale, Faith Tsirani. Atamuona, Samuel mtima udadumpha mpaka adapempha mnzakeyo kuti adzabwere ndi Faith kwawo, koma zidakanika. Patapita … The post Tidakumana Bwanji appeared first on Nation Online.
This is a summary. Read the full article at the original source.

